Chinenero chamakono: ny Chichewa

Zinenero
Selected Language:

Mudzi - Mabuku - Nyambo ya Satana

Nyambo ya Satana
Mphunzitsi: John Bevere
Akupezeka m’chinenero:

Nyambo ya Satana imayika poyera china choposa pa zokola zimene mdani amagwiritsa ntchito kuchotsa okhulupirira ku chifuniro cha Mulungu: chokhumudwitsa. Anthu ambiri akoledwa ndi msampha umenewu ndipo sadziwa nkomwe.

Usanyengedwe! Kristu anati, “Ndikosatheka kuti chokhumudwitsa chisabwere” (Luka 17:1). Sungasankhe kukhumudwitsidwa kapena kusakhumudwitsidwa, koma ukhoza kusankha mmene ungachitire ndi chokhumudwitsa. Ukachigwira bwino chokhumudwitsa, udzakhala wolimba kuposa kuwawidwa. Kachitidwe kabwino kokha kadzakupangitsa kukhala ndi ubale wosagwedezeka ndi Mulungu.

Kubzolera mu uthenga uwu, John Bevere adzakupatsa mphamvu yokhalabe mu chifuniro cha Mulungu ndi kumasuka ku kukayikitsa ndi kusakhulupirika. Ukhoza kuthawa maganizo okhala wokhudzidwa ndi kukhala wopanda mtolo wakupsya mtima ndi kutaya mtima. Pamene ukupeza mlingo wa pamwamba wodzipereka kwa Mulungu, moyo wako udzadzazidwa ndi chikhululukiro, chiyanjano, ndi chimwemwe chochulukira-chulukira.

Tengani (~1.78 MB)

Gawirani pa